Upepese, apo bii ndichita china chake – Zani Challe waopseza Tuno

…Tuno akuloza chala mowa omwe anamwa Kuli chinkulirano pakati pa oyimba Zani Challe yemwe lero watulutsa chikalata chomuuza oyimba Tuno kuti amupepese apo bii apanga chinthu china chomwe sananene ati kamba komunena kuti iye amagulitsa thupi komaso amachita malonda a mankhwala ozunguza ubongo. Nkhaniyi yayamba Lachiwiri usiku pomwe Tuno yemwe anabadwa Tunosiwe Mwakalinga amacheza mu […]

The post Upepese, apo bii ndichita china chake – Zani Challe waopseza Tuno appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください