Unduna woona za Ulimi watulutsa mitengo yogulira mbewu

Boma kudzera muunduna owona za Ulimi m’dziko muno watulutsa mitengo yoyambira kugula mbewu ya chaka chino ndipo mwazina Chimanga chizigulidwa pamtengo wa K650 pa kilogiramu. Izi ndi malingana ndi chikalata chomwe undunawu watulutsa lachinayi pa 4 April 2024 kudzera kwa mlembi mu undunawu a Dickxie Kampani. Mitengo yogulira mbewu zina ili motere: Soya K800, Mpunga […]

The post Unduna woona za Ulimi watulutsa mitengo yogulira mbewu appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください