Unduna wati pali chiopsezo cha madzi osefukira ku mpoto

Unduna Woona za Madzi ndi Ukhondo wati kuyambira pa 7 mpaka pa 14 mwezi uno, madera ambiri kumpoto kwa dziko lino komanso m’mbali mwa nyanja, akhalabe akulandira mvula yamphamvu, zomwe zikupeleka chiopsezo choti kumaderawa kutha kukhala madzi osefukira. Izi ndi malinga chikalatachi chomwe unduna watulutsa chomwe wasainira ndi m’modzi mwa akuluakulu ake a James Chitete […]

The post Unduna wati pali chiopsezo cha madzi osefukira ku mpoto appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください