Pomwe pali chiopsezo cha njala yadzaoneni, unduna wa Zamalimidwe walangiza anthu kuti ayesetse kulima chimanga komaso mbewu zina m’madimba ndipo wachenjeza kuti uthana ndi mchitidwe oberana komaso kugulitsa chimanga ndi mbewu zina zisanakhwimitsitse komanso zinakali m’munda. Izi ndi malingana ndi kalata yomwe undunawu watulutsa yomwe wasainira ndi Dickxie Kampani yemwe ndi mlembi mu unduna wa […]
The post Unduna wati alimi asagulitse chimanga chinakali m’munda appeared first on Malawi 24.