Pamene madera ambiri dziko lino akhudzidwa ndi vuto losowa mvula yokwanira, pali chiopsezo choti dziko lino likhala lopanda chakudya chokwanira chaka cha mawa. Koma akatswiri pa nkhani za ulimi ati boma likuyenera kulimbikitsa alimi kuti azichita ulimi wa mthilira komanso alangiza alimi dziko lino kutsatira njira za makono za malimidwe ndi kugwiritsa ntchito mbeu zosachedwa […]
The post Ulimi wa mthilira ndi omwe ungapulumutse Malawi ku vuto lakusowa kwa chakudya, atero akatswiri appeared first on Malawi 24.