Ulendo wa achinyamata omwe amayenera kunyamuka lero lachitatu kupita mdziko la Israel wasinthidwa. Achinyamata okwana 200 omwe amayenera kukwera ndege lero pa bwalo la ndege la Kamuzu International ku Lilongwe ulendo okagwira ntchito ku Minda ya mdziko la Israel wasinthidwa. Malinga ndi uthenga omwe Malawi24 yapeza kuchokera ku bugwe lomwe likuyendetsa za izi la Lions […]
The post Ulendo wa ku Israel wasintha appeared first on Malawi 24.