A Martha Chizuma omwe ndi mkulu wabungwe lothana ndi katangale la Anti-Corruption Bureau (ACB) ati utsogoleri wa a Lazarus Chakwera waonetsa chidwi chothana ndi katangale m’dziko la Malawi. Mkulu wabungweli amayankhula izi ku nkumano omwe umachitika dzulo mu mzinda wa Lilongwe ku BICC okhudza zakatangale. Iwo anati pa zaka 25 zomwe bungweli lakhala likutumikira m’dziko […]
The post Ulamuliro wa a Chakwera waonetsa chidwi chothana ndi katangale, atero a Chizuma appeared first on Malawi 24.