Mkhala kale pa ndale, Uladi Mussa, wapempha nthumwi ku msonkhano waukulu wa chipani cha MCP kuti zikavomereze dzina la mtsogoleri wadziko lino a Lazarus Chakwera kuti adzaimilenso chipanichi pa chisankho cha chaka chamawa. Polankhula ndi olemba nkhani mumzinda wa Lilongwe, a Mussa ati utsogoleri wa a Chakwera waonetselatu kuti ndi umene ungatulule dziko lino. […]
The post Uladi Mussa wapempha nthumwi za MCP kuti ‘chonde, chonde, kavomerezeni Chakwera azayimilenso’ appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.