‘Tulutsani wanuyo timuone: ngati ali nkhalamba, ife wathu ndi mnyamata’ – wakhazikitsa chipani Nankhumwa

Kuli kanthu mu 2025. Chipani cha People’s Development Party (PDP) chakhazikitsidwa tsopano ndipo a Kondwani Nankhumwa abwela poyera: iwo akutsogolera chipanichi ndipo 2025 akulowa m’boma basi. Inu mufune, kaya musafune. Poyankhula pa mwambo okhadzikitsa chipanichi omwe wachitikira mu boma la Blantyre, a Nankhumwa ati iwo tsopano athana nazo basi za DPP, tsopano azipanga za PDP. […]

The post ‘Tulutsani wanuyo timuone: ngati ali nkhalamba, ife wathu ndi mnyamata’ – wakhazikitsa chipani Nankhumwa appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください