Vuto lakusowa kwa sugar ku Malawi likuyembekezeka kutha pamene kampani ya Salima Sugar yalengeza kuti tsopano ili ndi sugar okwanira kufikira m’madera ambiri m’dziko muno. Sitolo za Ekhaya, Shoprite, Chipiku, Sana, ndi zina zikuluzikulu zakhala zisakupezeka ndi sugar okwanira m’dziko lino koma tsopano iz zikuyembekezeka kusitha. Kudzera mwa kampani yowatumikira kuperekera katundu wawo, a Salima […]
The post Tulutsani makapu tsopano, a Salima ati kukubwera Suga ngambwingambwi appeared first on Malawi 24.