Katswiri oyimba nyimbo zachamba cha afro pop, Dan Lufani, yemwe amadziwika ndi dzina loti Dan Lu wauza mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera kuti alephera kulamulira ndipo atule pansi udindo. Izi ndi malingana ndi nyimbo yatsopano yomwe Dan Lu watulutsa lachitatu pa 23 March yomwe mutu wake waipatsa kuti ‘Tulani pansi’ ndipo ikulamula kuti […]
The post ‘Tulani pansi’ – Dan Lu wauza Chakwera appeared first on Malawi 24.