Yalimba nkandilo! Pomwe a Kondwani Nankhumwa, a Grezelder Jeffrey komanso a Cecilia Chazama amafuna bwalo la apilo liwabwezeretse pa maudindo awo mu chipani chotsutsa boma cha Democratic Progressive (DPP) komaso kuwapatsa chiletso kuti asakaonekere ku komiti yosungitsa mwambo mchipani, bwaloli lakana mapemphowa ndipo atatuwa akuyeneraso kupeleka ndalama zomwe zagwiritsidwa ntchito pakumva mlanduwu. Atatuwa anakamang’ala ku […]
The post Tsoka likalimba: Bwalo la apilo lakanaso Nankhumwa, Jeffrey appeared first on Malawi 24.
Moni Malawi 
