Tseketseke a Laz abwera

Lazalo muliyenda Atakhala kunja kwa Mwezi, kuombedwa mphepo zina mmizinda ya ku Kenya, America ndi UAE, mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera afika kumudzi tsopano. Ndipo abwela ndi chithumba chimene chikuyembekezereka kuthetsa mavuto a kusowa kwa mafuta, kuzimazima kwa magetsi ndi chipwirikiti pa za chuma. A Chakwera anachoka ku Malawi pa 12 Mwezi watha […]

The post Tseketseke a Laz abwera appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください