Tony Ngalande akhazikitsa ntchito yogulitsa chimanga m’misika yoyendayenda

Phungu wa nyumba yamalamulo wa dera la kumpoto m’boma la Balaka, Tony Ngalande, wakhazikitsa ndondomeko yogulitsa chimanga cha bungwe la boma logulitsa mbewu la Admarc kudzera mu misika yoyendayenda. A Ngalande adauza nyumba yofalitsa nkhani ya Malawi24 loweluka m’mawa kuti aganiza zokhazikitsa ntchitoyi ndi cholinga chochepetsa mtunda umene anthu amayenda kupita ku msika waukulu wa […]

The post Tony Ngalande akhazikitsa ntchito yogulitsa chimanga m’misika yoyendayenda appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください