Tony Ngalande akhazikitsa mpikisano wa masewero msukulu za pulayimale

Phungu wa nyumba ya malamulo wa dera la kumpoto m’boma la Balaka olemekezeka a Tony Ngalande ati ndi Khumbo lawo kuthandizira kutukula masewero osiyanasiyana pakati pa achinyamata komanso ophunzira msukulu za pulayimale. A Ngalande ayankhula izi lachisanu pamene amakhazikitsa chikho cha mpikisano wa mpira wa miyendo komanso manja chomwe ma timu ochokera msukulu zosiyanasiyana m’boma […]

The post Tony Ngalande akhazikitsa mpikisano wa masewero msukulu za pulayimale appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください