Tonse yakanika kutumikira a Malawi, iyambe kupakila, chatero chipani cha DPP

Chipani chotsutsa boma cha DPP chati ulamuliro wa mgwirizano wa Tonse uyambe kuchotsera masiku ake okhala m’boma kaamba koti alephera kutumikira a Malawi. Gavanala wachipanichi mchigawo chakumvuma Sheikh Imran Ntenje wati umoyo wa nzika ukupitilira kukhala wa umphawi mu zaka zinayi zomwe utsogoleriwu walamulira dziko lino. Sheikh Ntenje wati katundu ofunikira monga chimanga, sugar komanso […]

The post Tonse yakanika kutumikira a Malawi, iyambe kupakila, chatero chipani cha DPP appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください