Bright Msaka yemwe ndi phungu wa DPP ku Machinga Likwenu wati anthu ambili mdziko muno sakukwanitsa kudya katatu monga momwe zimayenera kukhalira malingana ndi malonjezano omwe boma la mgwirizano wa Tonse lidalonjeza a Malawi mmbuyomu. Izi zanenedwa pomwe aphungu akupitirizabe kuikapo ndemanga zawo pa ndondomeko ya za chuma ya chaka chino yomwe inaperekedwa ku nyumba […]
The post Tonse Alliance ndi ya bodza: Palibe akudya katatu mu Malawi muno, atero a Bright Msaka appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.