Tomato atha kukhala golide wathu – atelo akatswiri

…boma alipempha kupeza misika yokhazikika Akatswiri a zaulimi ati ngati ulimi wa tomato ungatengedwe bwino komaso ngati pangakhale njira zamakono zosungira tomato, mbewuyi itha kumabweretsa ndalama zakunja zochuluka kuposa fodya yemwe dziko lino limadalira pano. Izi zikubwera pomwe misika yochuluka m’dziko muno yalandira phwetekele opitilira muyezo zomwe zapangitsa kuti mitengo ya mbewuyi ikhwefuke kwambiri kufika […]

The post Tomato atha kukhala golide wathu – atelo akatswiri appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください