Yemwe akufuna kudzayima nawo pa chisankho cha mtsogoleri wa dziko lino, a Milward Tobias, wauza mtsogoleri wa dziko lino, Dr. Lazarus McCarthy Chakwera, kuti afunsire nzeru kwa anthu ena pa mmene angathanirane ndi mavuto a zachuma omwe akuta dziko lino. A Tobias, omwe ndi katswiri pa nkhani za chuma, ati mavuto a za chuma omwe […]
The post Tobias auza Chakwera zina mwa njira zokonzera chuma appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.