Patangopita masiku ochepa kampani ya lamya za m’manja ya Airtel Malawi itakweza mitengo yogulira ma bandulo ake, nayonso TNM yakweza mitengo yake ndi K20 pa K100 iliyonse. Malingana ndi uthenga omwe kampaniyi yatulutsa yati yachita izi kutsatira kugwa kwa mphamvu ya ndalama ya kwacha. Mwachitsanzo Pamtsetse bundle wa masiku 7 yemwe amagulidwa pa mtengo wa […]
The post TNM yakweza mitengo ya mabandulo ake oimbira komanso a intaneti appeared first on Malawi 24.