Tiyeni tipempherere mvula, latero bungwe la EAM

Bungwe la Evangelical Association of Malawi (EAM) lapempha anthu onse dziko muno kuti pakhale mapemphero apaderadera opemphelera mvula kamba ka ng’amba yomwe yakhudza m’dera ambiri m’dziko muno. Chikalata chomwe wasainira ndi mlembi wamkulu m’bungweli, M’busa Francis Mkandawire,   chikumeneza anthu onse dziko muno posatengera chipembedzo kutenga nawo gawo mapempherowa kuti mvuLa iyambeso kugwa moyenera. “Tipempere ma […]

The post Tiyeni tipempherere mvula, latero bungwe la EAM appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください