A Malawi omwe amafuna kuboola mtambo koma anakhudzidwa ndi kusokonekera kwa sisitimu ya nthambi yoona za anthu olowa ndi kutuluka ya DICS, atha kuusa moyo tsopano poti nthambiyi yati yayambiraso kusindikiza komaso yatsitsa mtengo wa ziphaso zoyendera. Sisitimu ya DICS inasokonekera m’mwezi wa January chaka chino ndipo zakhala zikuveka kuti akathyali ena ndi omwe anapanga […]
The post Tiyeni konko! sisitimu ya immigration yabwezeretsedwa, ziphaso zatsika mtengo appeared first on Malawi 24.