Tithandiza anthu amene ali ndi vuto la njala, yatero banki ya NBS

Banki ya NBS yalonjeza kuthandiza anthu amene akhudzidwa ndi njala dziko muno. Mkulu wa nthambi ya bankiyi ku Limbe, Twaibu M’nani, anayankhula izi dzulo pa 18 February, 2024, m’boma ya Chiradzulu kumene bankiyi imagawa ufa wa chimanga wa ndalama zokwana 3.5 miliyoni ku maanja 150 amene akhudzidwa ndi vuto la njala. Mu mau ake, mfumu […]

The post Tithandiza anthu amene ali ndi vuto la njala, yatero banki ya NBS appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください