Tisiyileni Buluma timuthyole khosi – achinyamata a MCP

Mdima umene a Malawi ena anauona mu utsogoleri wa chipani cha MCP wayandikanso pamene a chinyamata a chipanichi ati akufuna kupha Helen Buluma. Malinga ndi mchezo wa pa makina a Intaneti a WhatsApp umene wafala pa bwalo la Fesibukhu, achinyamata ena a mu MCP akuona kuti Mayi Buluma akuyenda atafa kale. Izi amakambilana Mayi Buluma […]

The post Tisiyileni Buluma timuthyole khosi – achinyamata a MCP appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください