Tisaleme kuthandiza anthu omwe akhudzidwa ndi njala – atero mai Joyce Banda

Mtsogoleri wakale wa dziko lino, a Joyce Banda, apempha boma ndi mabungwe omwe akugawa chimanga kwa anthu omwe akhudzidwa ndi njala m’dziko muno kuti achite machawi kufikira madera ambiri anthu ambiri akhudzidwa ndi mavuto osowa chakudya. A Banda anayankhula izi ku Domasi boma la Zomba kumene anali nawo pa mwambo omwe bungwe la Shepperd Bushiri […]

The post Tisaleme kuthandiza anthu omwe akhudzidwa ndi njala – atero mai Joyce Banda appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください