Msonkhano waposachedwapa wa UTM, umene unachitikira ku Mzuzu ndipo ndikusankha Dr. Dalitso Kabambe kukhala mtsogoleri wa chipanichi, wasiya anthu ambiri atamangidwa mphukusi. Msokhanowu, maka zotsatila za zisankhozi zadzetsa mafunso ambiri omwe mpaka pano mayankho zakupezeka. Enafe sitinali muchpinda momwe msonkhanowu umachitikira poti sitinali ma deligeti, koma tili panja tinamvako kuti magetsi anali vuto maka mmene […]
The post Tinayenda bwanji ku Mzuzu? Kusanthula msonkhano wosankha atsogoleri ku UTM appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.