Amayi omwe adali mdziko la Oman komwe anapita atanamizidwa kuti adzikapatsidwa malipilo ochuluka, achenjeza atsikana ena kuti asamakhumbileko ponena kuti ku dzikoli kuli ukapolo osasimbika, ndipo wina waulura kuti wakhala akugwililidwa ndi bwana komaso anzake a bwana wake. Zaka zingapo zapitazo makamaka kuyambira chaka cha 2021, m’masamba a nchezo mwakhala mukuyenda nkhani ya asungwana omwe […]
The post Tinali akapolo, ndagwililidwa ndi amuna angapo – amayi aulura nkhaza za ku Oman appeared first on Malawi 24.