Timu yampira wa miyendo ya azibambo imakondeledwa — watero Tabitha

Mtsogoleri wa timu ya mpira wa miyendo ya dziko lino yomwe osewera ake ali azimayi, Tabitha Chawinga, wadandaula ndikusowa chithandizo choyendesera timuyi. Chawinga wauza nyuzipepala ya Nation kuti dziko lino lilibe chidwi chotukula mpira wa azimayi komanso wadandaula ndikukondeledwa kwa timu ya azibambo. Tabitha wanena izi posatira kulengezedwa koti timu ya azimayi itha osatenga nawo […]

The post Timu yampira wa miyendo ya azibambo imakondeledwa — watero Tabitha appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください