Nduna yofalitsa nkhani a Moses Kunkuyu ati ndiokonzeka kukachingamila mtolankhani Gregory Gondwe ku bwalo la ndege pofuna kusonyeza kuti boma lilibe mangawa ndipo kuti a Gondwe ndi mfulu kubwelela Ku Malawi. A Kunkuyu auza atolankhani Ku Lilongwe lero kuti pomwe a Gondwe amatuluka m’dziko muno kudzela Ku bwalo la ndege Ku Lilongwe, boma limadziwa komanso […]
The post Tilibe mangawa ndi Gregory Gondwe, akuchocha kuzera Lilongwe timadziwa, akamabwera ndili okonzeka kukamulandira, atero a Kunkuyu appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.