Tili ndi masomphenya okonza mphamvu za magetsi patokha — yatero kampani ya Illovo

Kampani yopanga shuga m’dziko muno ya Illovo yalengeza kuti ili ndi masomphenya okonza mphamvu za magetsi payokha kuti ichepetse ndalama zimene kampaniyi imaluza kulipira magetsi ku ESCOM. Mkulu wa kampaniyi, Lekani Katandula, ndiye anayankhula izi lero mu mzinda wa Blantyre pamene anali ndi nkumano ndi anthu ena amene amathandizira kuyendetsa ntchito za kampaniyi. “Masomphenya wa […]

The post Tili ndi masomphenya okonza mphamvu za magetsi patokha — yatero kampani ya Illovo appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください