Tikutumiza chimanga chochepa dala pofuna kuteteza ku mbava – Sam Kawale

Nduna yowona za malimidwe a Sam Kawale ati boma likhala likupitiliza kutumiza chimanga chimene likusunga mu nkhokwe zake ku misika ya ADMARC m’dziko muno ngakhale anthu pakali pano ayamba kukolola chimanga m’minda yawo madela ena. A Kawale amayankhula izi m’nyumba ya malamulo pamene Phungu wa nyumba ya malamulo ku m’mawa kwa boma la Chiradzulu anafunsa […]

The post Tikutumiza chimanga chochepa dala pofuna kuteteza ku mbava – Sam Kawale appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください