Zitsulo kunolana: Oyimba Giboh Pearson walangiza oyimba nzake Joe Gwaladi kuti achepetse uchidakwa, ndipo wamuuza kuti asankhe kumetengera ku mapemphero kapena kwa sing’anga. Nkhaniyi yadza potsatira kanema yemwe anthu akugawana m’masamba anchezo yomwe ikuonetsa Gwaladi atapana mkazi pa malo ena omwela chakumwa cha ukali. Mu kanemayo, Gwaladi yemwe amaoneka kuti wandongwa, akuoneka akugwiragwira mabere a […]
The post “Tikupititse kwa sing’anga kapena ku mapemphero?” – Gibo Pearson wakwiyira Gwaladi appeared first on Malawi24.