Tikumangani mukamafalitsa kuti Kunkuyu akukhuzidwa ndi imfa ya Witika – atelo apolisi

Apolisi m’dziko muno ati amanga aliyese amene apitilire kufalitsa nkhani zonama kuphatikiza yoti nduna yofalitsa nkhani a Moses Kunkuyu akukhudzidwa ndi kuphedwa kwa Allan Witika mwezi watha. Izi zili muchikalata chomwe nthambi ya yosungitsa chitetezoyi ya Malawi Police Service (MPS) yatulutsa lolemba pa 23 October, 2023 chomwe wasainira ndi ofalitsa nkhani wa nthambiyi a Peter […]

The post Tikumangani mukamafalitsa kuti Kunkuyu akukhuzidwa ndi imfa ya Witika – atelo apolisi appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください