Tikudutsa muzowawa: Escom yapempha kukwezedwa mtengo kwa magetsi

Pamene anthu m’dziko muno akupitilira kudandaula za zikhomo pankhani ya zachuma, kampani yogulitsa magetsi ya Electricity Supply Corporation of Malawi (ESCOM) yati ikufuna mtengo wa magetsi ukwere apo bii kampaniyi itsekedwe kaye. Izi ndi malingana ndi mkulu wakampaniyi a Kamkwamba Kumwenda omwe amayankhula lachiwiri pamsonkhano wa atolankhani omwe unachitikira kumaofesi akampaniyi mumzinda wa Blantyre. A […]

The post Tikudutsa muzowawa: Escom yapempha kukwezedwa mtengo kwa magetsi appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください