Monga nyimbo ya mtsogoleri wakale wa dziko lino malemu Bingu wa Mutharika inkanenera, mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera apempha mayiko osaukitsitsa pa dziko la pansi kuti ayende limodzi ndi mtima umodzi. A Chakwera ayankhula izi pachiweru pomwe anatenga nawo gawo pa zokambirana za atsogoleri a mayiko osaukitsitsa pa dziko lonse la pansi omwe […]
The post Tigwirane manja: Chakwera apempha maiko osauka kuti ayende limodzi ndi mtima umodzi appeared first on Malawi24.