A Griffin Maruwasa, omwe ndi wachiwiri kwa mtsogoleri wa chipani cha ndale chomwe chikhadzikitsidwe posachedwapa cha Economic Freedom Party (EFP) atsindika kuti chipani chawo chidzawonetsetsa kuti voti ya anthu ikulemekezedwa. A Maruwasa anena izi poyankhulana ndi Malawi24 pakutha pa mkumano omwe adali nawo ndi mamembala a chipanichi m’boma la Balaka. Iwo adati kwa nthawi yaitaili, […]
The post Tidzalemekeza voti ya aliyense – chatero chipani cha EFP appeared first on Malawi 24.
Moni Malawi 