Ngati muli bwenzi wa ziwaya za nyama mu Lilongwe, ndi kutheka munadya kale galu wanu. Maka anthu amene mumakonda kubaya ya mbuzi. A polisi mu mzinda wa Lilongwe amanga bambo Andrew Mthiko a zaka 38 kamba kowaganizira kuti akhala akudyetsa ma kasitomala awo nyama ya galu kumati ndi ya mbuzi. Malinga ndi maripoti ochoka ku […]
The post Tibaye nawo galu – wamangidwa ku Lilongwe kamba kogulitsa kanyenya wa galu appeared first on Malawi24.