Thambo lagwa Ku Nigeria pamene katswiri opanga kanema wazisudzo watisiya

Mdima wagwanso m’dziko la Nigeria pamene katakwe opanga mafilimu yemwe dzina lake ndi Amaechi Mounagor wadziwika kuti wamwalira atadwala nthenda ya impso. Izi zikudza pasanathe mwezi dzikoli litatayanso katswiri wina a John Okafor yemwe amadziwika bwino ndi dzina loti Mr Ibu kumayambiliro a mwezi uno. Mmasiku apitawo a Mounagor adabwera poyera kwa anthu aku Nigeria […]

The post Thambo lagwa Ku Nigeria pamene katswiri opanga kanema wazisudzo watisiya appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください