…Bullets yakanika kuzemba pa Mazembe Zikakhala nyerere zikuti ndi chifukwa kunalibe ma ref ogulitsa, eni ake a Bullets ati bola anafikako ku CAF. Koma lero pa 30 Sepitemba ulendo wa Bullets watha basi. Mazembe ya Joseph Kamwendo yachita chobaya. Kulasa mu nthiti akazembe a dziko lino anga ndi a gwape. Pa masewero achiwiri amene anachitika […]
The post Tembenuza galeta andilasa! Ulendo wa CAF wathera pamebepa appeared first on Malawi 24.