Tavomera ndipo zatha basi – yagonja Wanderers

Timu ya mpira wa miyendo ya Mighty Mukuru Wanderers, yati yavomeleza chilango chomwe yapatsidwa ndi bungwe la Football Association of Malawi (FAM) ndipo yati siyipangaso apilu. Izi zikudza pomwe komiti yomva ma apilu (appeal) ku bungwe la FAM Lachinayi yatulutsa chigamulo pa nkhani yomwe timu ya Wanderers inakadandaula italephera kukhutitsidwa ndi chigamulo cha komiti yoyendetsa […]

The post Tavomera ndipo zatha basi – yagonja Wanderers appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください