Tamia Ja amangidwa poganiziridwa kuti anazembeyesa K8 miliyoni ya mwini

Apolisi munzinda wa Lilongwe amanga mmodzi mwa anthu odziwika bwino pamasamba amchezo Hannah Jabes, yemwe amadziwika bwino ndi dzina la Tamia Ja, kamba kankhani yogwirizana ndi kuba. Malingana ndi a polisi, masiku angapo apitawo analandira dandaulo kuchokera kwa mkulu wina wochita malonda yemwe anati Tamia Ja anazambayitsa ndalama zokwana 8 million kwacha zitaikidwa molakwika mu […]

The post Tamia Ja amangidwa poganiziridwa kuti anazembeyesa K8 miliyoni ya mwini appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください