Sukula ya sekondale ya Msiki m’boma la Mzimba ikusimba lokoma potsatira thandizo lokwanira 4.3 miliyoni lalandira kuchokera kwa ophunzira akale pa sukulu yaukachenjede ya Mzuzu. Masiku anayi apitawo, ophunzira akale pa Mzuzu University anadzidzimutsa sukulu ya Msika ndi thandizo la mabuku olemberamo komanso ndalama zimene zigwire ntchito ngati sukulu fizi kwa ana khumi ndi asanu. […]
The post Sukulu ya Msika iwomboledwa ndi ophunzira akale pa Mzuzu University appeared first on Malawi 24.