Bungwe la sukulu zoyima pazokha zophunzitsa anthu kuyendetsa galimoto, lati ganizo loti nthambi ya apolisi m’dziko muno itsekule sukulu yophunzitsa anthu kuyendetsa galimoto, ndilolakwika ponena kuti liwaphera nsika. Nkhaniyi ikudza pomwe posachedwapa nthambi ya polisi m’dziko muno yalengeza kuti ili kalikiliki ndimadongosolo ofuna kukhazikitsa sukulu komwe aziphunzitsa anthu kuyendetsa magalimoto amtundu osiyanasiyana. Malingana ndi ofalitsa […]
The post Sukulu ya apolisi yaoyendetsa galimoto yautsa mapokoso appeared first on Malawi 24.