Bungwe lomwe limawona za madzi mchigawo chakum’mwera la Southern Region Water Board (SRWB) lati anthu ena omwe akumalumikizilidwa madzi mwaulele sakulipira ma bilu a madzi chifukwa akumayesa kuti madziwo adzimwanso ulele Wofalitsa nkhani ku Bungwe la SRWB Rita Makwangwala ndiyemwe wayankhula izi ku Salima pansonkhano wapa chaka wa atolankhani a Bungwe la Zomba Press Club. […]
The post SRWB yati anthu ena amene analumikizilidwa madzi mwaulele sakulipira ma bilu appeared first on Malawi 24.