SRWB imanga damu lamakono ku Domasi m’boma la Zomba

Bungwe la Southern Region Water Board (BWB) yati ili ndi chikonzero chomanga dam lalikulu ku Domasi m’boma la Zomba limene lithandizire kuonjezera madzi amene bhodiyi imagawa komanso kuthandizira pa ulimi wa mthilira, ulimi wa nsomba komaso kupanga mphamvu za magetsi. Mneneri wa BWB,  Ritta Makwangwala, wati kupatula kuonjezera kugawa madzi mu chigawo cha kum’mwera, damuli […]

The post SRWB imanga damu lamakono ku Domasi m’boma la Zomba appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください