Kutsatira mpungwepungwe omwe wadza kamba koti a Lazarus Chakwera asintha dzina la chipatala cha Phalombe kukhala John Chilembwe Hospital, m’modzi mwa anthu omwe amayankhulapo pa zochitika m’dziko muno a Wonderful Mkhutche ayankhula moyikira kumbuyo a Chakwera ponena kuti sizachilendo kusintha dzina. Katswiriyu wayankhula izi pamene a Malawi ena akutsutsana ndi ganizo lomwe mtsogoleri wa dziko […]
The post Sizachilendo kusintha dzina, watero katswiri wina appeared first on Malawi 24.