Wapampando wa bhodi ya Mulhako wa Alhomwe watsutsa mphekesera yoti bhodiyi yachotsa mtsogoleri wakale wa dziko lino a Peter Mutharika ngati woyang’anira bungweli. Mukuyankhula kwawo pa msonkhano wa atolankhani mu mzinda wa Blantyre lachiwiri, Muchanakwaye Mpuluka yemwe ndi wapampando wa bhodiyi anati dongosolo ndi mphamvu zochotsa komaso kubwezeretsa amdindo mu bungweli zili ndi bhodi yaikulu […]
The post Sitinawachotse a Mutharika, latero bungwe la Mulhako appeared first on Malawi 24.