Ma bishopu a mpingo wa Katolika pansi pa bungwe la Episcopal Conference of Malawi (ECM), ati zomwe alamula kuti a nsembe asamapeleke mdalitso uli onse kwa anthu okwatilana amuna kapena akazi okhaokha, sizikutanthauza kuti iwo awukira mtsogoleri wa mpingowu Papa Francis. Sizikutanthauza kuti mpingowu waloleza maukwati a amuna kapena akazi okhaokha ndipo anenetsa kuti palibe […]
The post Sitinaukile – atelo mabishopu a Katolika ku Malawi appeared first on Malawi 24.