Pamene timu ya dziko lino yanyamuka kukagwebana ndi timu ya dziko la Liberia mundime yodzipezera malo mumpikisano wa dziko lose, mphunzitsi watimuyi Patrick Mabedi wati zokozekera sizinayende bwino koma wati akayesetsa mwa mtima bii. Timu ya Flames yanyamuka lolemba munzinda wa Lilongwe kupita m’dziko la Liberia komwe ikasewere ndi timu ya dzikolo lachisanu pa 17 […]
The post Sitinakonzekele bwino – wadandaula Mabedi appeared first on Malawi 24.