Anthu oyenda maulendo a pakati pa Lilongwe ndi Blantyre tsopano adzikhala ndi chisankho cha mayendedwe awo pomwe boma lalengeza kuti maulendo a sitima yapamtunda ayambiraso pakati pa mizinda iwiriyi. Izi ndi malingana ndi nduna yowona za mtengatenga ndi mtokoma a Jacob Hara omwe anena izi Lolemba munzinda wa Lilongwe. A Hara ati nkhaniyi ikutsatira kukonzedwa […]
The post Sitima iyambiraso kuyenda pakati pa Lilongwe ndi Blantyre appeared first on Malawi 24.